2 Mbiri 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Yehova sanafune kuwononga nyumba ya Davide chifukwa cha pangano limene anachita ndi Davide,+ poti anamulonjeza kuti adzamʼpatsa nyale nthawi zonse, iyeyo ndi ana ake.+
7 Koma Yehova sanafune kuwononga nyumba ya Davide chifukwa cha pangano limene anachita ndi Davide,+ poti anamulonjeza kuti adzamʼpatsa nyale nthawi zonse, iyeyo ndi ana ake.+