2 Mbiri 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mʼmasiku a Yehoramu, Aedomu anagalukira Yuda+ ndipo kenako anasankha mfumu yoti iziwalamulira.+