-
2 Mbiri 21:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Choncho Yehoramu ndi akuluakulu a asilikali ake anapita kumeneko pamodzi ndi magaleta ake onse. Ndiyeno ananyamuka usiku nʼkukapha Aedomu amene anamuzungulira komanso atsogoleri a asilikali okwera magaleta.
-