2 Mbiri 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Aedomu akupitirizabe kugalukira Yuda mpaka lero. Pa nthawi imeneyinso Libina+ anagalukira Yehoramu chifukwa Yehoramuyo anali atasiya Yehova Mulungu wa makolo ake.+
10 Koma Aedomu akupitirizabe kugalukira Yuda mpaka lero. Pa nthawi imeneyinso Libina+ anagalukira Yehoramu chifukwa Yehoramuyo anali atasiya Yehova Mulungu wa makolo ake.+