2 Mbiri 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komanso iye anamanga malo okwezeka+ mʼmapiri a ku Yuda zomwe zinachititsa kuti anthu a ku Yerusalemu achite uhule wauzimu ndipo iye anasocheretsanso Yuda.
11 Komanso iye anamanga malo okwezeka+ mʼmapiri a ku Yuda zomwe zinachititsa kuti anthu a ku Yerusalemu achite uhule wauzimu ndipo iye anasocheretsanso Yuda.