2 Mbiri 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako analandira kalata yochokera kwa mneneri Eliya+ yakuti: “Yehova Mulungu wa Davide kholo lanu wanena kuti, ‘Sunayende mʼnjira za Yehosafati+ bambo ako kapena mʼnjira za Asa+ mfumu ya Yuda.
12 Kenako analandira kalata yochokera kwa mneneri Eliya+ yakuti: “Yehova Mulungu wa Davide kholo lanu wanena kuti, ‘Sunayende mʼnjira za Yehosafati+ bambo ako kapena mʼnjira za Asa+ mfumu ya Yuda.