-
2 Mbiri 21:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Iweyo udzadwala matenda ambiri kuphatikizapo matenda amʼmatumbo, mpaka matumbo ako azidzatuluka tsiku ndi tsiku chifukwa cha matendawo.’”
-