2 Mbiri 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho iwo anafika mwamphamvu mpaka analowa mu Yuda. Anthuwo anatenga katundu yense amene anali mʼnyumba ya mfumu+ komanso ana ake ndi akazi ake. Sanamusiyire mwana aliyense kupatulapo Yehoahazi,*+ mwana wake wamngʼono kwambiri.
17 Choncho iwo anafika mwamphamvu mpaka analowa mu Yuda. Anthuwo anatenga katundu yense amene anali mʼnyumba ya mfumu+ komanso ana ake ndi akazi ake. Sanamusiyire mwana aliyense kupatulapo Yehoahazi,*+ mwana wake wamngʼono kwambiri.