2 Mbiri 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Patatha zaka ziwiri zathunthu akudwala, matumbo ake anatuluka chifukwa cha matendawo ndipo matenda atafika poipa kwambiri, iye anamwalira. Anthu ake sanawotche zonunkhira pa maliro ake ngati mmene anachitira pa maliro a makolo ake akale.+
19 Patatha zaka ziwiri zathunthu akudwala, matumbo ake anatuluka chifukwa cha matendawo ndipo matenda atafika poipa kwambiri, iye anamwalira. Anthu ake sanawotche zonunkhira pa maliro ake ngati mmene anachitira pa maliro a makolo ake akale.+