2 Mbiri 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehoramu anakhala mfumu ali ndi zaka 32 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 8. Iye atafa, palibe amene anadandaula. Choncho anamuika mu Mzinda wa Davide,+ koma osati mʼmanda a mafumu.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:20 Nsanja ya Olonda,11/15/1998, tsa. 32
20 Yehoramu anakhala mfumu ali ndi zaka 32 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 8. Iye atafa, palibe amene anadandaula. Choncho anamuika mu Mzinda wa Davide,+ koma osati mʼmanda a mafumu.+