-
2 Mbiri 22:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova ngati mmene anachitira anthu a mʼbanja la Ahabu, chifukwa iwowo anakhala alangizi ake pambuyo pa imfa ya bambo ake ndipo anamʼpweteketsa.
-