2 Mbiri 22:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anatsatira malangizo awo ndipo anapita kunkhondo ndi Yehoramu mwana wa Ahabu mfumu ya Isiraeli, kukamenyana ndi Hazaeli+ mfumu ya Siriya ku Ramoti-giliyadi.+ Kumeneko oponya mivi anavulaza Yehoramu.
5 Anatsatira malangizo awo ndipo anapita kunkhondo ndi Yehoramu mwana wa Ahabu mfumu ya Isiraeli, kukamenyana ndi Hazaeli+ mfumu ya Siriya ku Ramoti-giliyadi.+ Kumeneko oponya mivi anavulaza Yehoramu.