2 Mbiri 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehu atayamba kupereka chiweruzo kwa anthu a mʼbanja la Ahabu, anapeza akalonga a Yuda ndi ana a abale ake a Ahaziya, omwe ankatumikira Ahaziya, ndipo anawapha.+
8 Yehu atayamba kupereka chiweruzo kwa anthu a mʼbanja la Ahabu, anapeza akalonga a Yuda ndi ana a abale ake a Ahaziya, omwe ankatumikira Ahaziya, ndipo anawapha.+