-
2 Mbiri 22:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kenako iye anayamba kufunafuna Ahaziya ndipo anthu anakamugwira ku Samariya kumene ankabisala nʼkupita naye kwa Yehu. Atatero iwo anamupha nʼkumuika mʼmanda+ popeza anati: “Uyu ndi mdzukulu wa Yehosafati yemwe anafunafuna Yehova ndi mtima wake wonse.”+ Panalibe aliyense wa mʼbanja la Ahaziya amene akanatha kukhala mfumu ya ufumuwo.
-