2 Mbiri 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Gulu lina lidzakhale panyumba ya mfumu,+ ndipo gulu lachitatu lidzakhale pageti lotchedwa Maziko. Anthu onse adzakhale pamabwalo a nyumba ya Yehova.+
5 Gulu lina lidzakhale panyumba ya mfumu,+ ndipo gulu lachitatu lidzakhale pageti lotchedwa Maziko. Anthu onse adzakhale pamabwalo a nyumba ya Yehova.+