-
2 Mbiri 23:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Iye anauza anthu onse kuti aimirire, aliyense atanyamula zida zake, kuyambira kumanja kwa nyumbayo mpaka kumanzere kwa nyumbayo, pafupi ndi guwa lansembe ndiponso pafupi ndi nyumbayo. Anazungulira mfumuyo kumbali zonse.
-