2 Mbiri 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ataliya atamva phokoso la anthu akuthamanga komanso kutamanda mfumu, nthawi yomweyo anapita kwa anthu amene anali panyumba ya Yehova.+
12 Ataliya atamva phokoso la anthu akuthamanga komanso kutamanda mfumu, nthawi yomweyo anapita kwa anthu amene anali panyumba ya Yehova.+