-
2 Mbiri 23:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma wansembe Yehoyada anatenga atsogoleri a magulu a asilikali 100, omwe anasankhidwa kuti aziyangʼanira asilikali, ndipo anawauza kuti: “Mʼchotseni pakati pa asilikali ndipo aliyense amene angamutsatire mumuphe ndi lupanga!” Wansembeyo anali atanena kuti: “Musamuphere mʼnyumba ya Yehova.”
-