-
2 Mbiri 23:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Kenako Yehoyada anapereka udindo woyangʼanira ntchito zapanyumba ya Yehova kwa ansembe ndi Alevi amene Davide anawaika mʼmagulu panyumba ya Yehova, kuti azipereka nsembe zopsereza za Yehova+ mogwirizana ndi zimene zinalembedwa mʼChilamulo cha Mose.+ Anawauza kuti azizipereka mosangalala poimba nyimbo motsatira malangizo amene Davide anapereka.
-