2 Mbiri 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anaikanso alonda apageti+ pafupi ndi mageti a nyumba ya Yehova kuti aliyense wodetsedwa mwa njira ina iliyonse asalowe.
19 Anaikanso alonda apageti+ pafupi ndi mageti a nyumba ya Yehova kuti aliyense wodetsedwa mwa njira ina iliyonse asalowe.