5 Choncho anasonkhanitsa ansembe ndi Alevi nʼkuwauza kuti: “Pitani mʼmizinda ya Yuda mukatolere ndalama kwa Aisiraeli onse kuti muzikonzera nyumba ya Mulungu wanu+ chaka ndi chaka. Muchite zimenezi mwachangu.” Koma Aleviwo sanachite zimenezo mwachangu.+