2 Mbiri 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pajatu ana a Ataliya+ mkazi woipa uja anathyola nyumba ya Mulungu woona,+ ndipo anagwiritsa ntchito zinthu zonse zopatulika zamʼnyumba ya Yehovayo potumikira Abaala.”
7 Pajatu ana a Ataliya+ mkazi woipa uja anathyola nyumba ya Mulungu woona,+ ndipo anagwiritsa ntchito zinthu zonse zopatulika zamʼnyumba ya Yehovayo potumikira Abaala.”