2 Mbiri 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako mfumuyo inalamula kuti apange bokosi+ nʼkuliika panja, pageti la nyumba ya Yehova.+