2 Mbiri 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atatero anauza anthu onse a ku Yuda ndi ku Yerusalemu kuti abweretse kwa Yehova msonkho wopatulika+ umene Mose mtumiki wa Mulungu woona analamula Aisiraeli mʼchipululu.
9 Atatero anauza anthu onse a ku Yuda ndi ku Yerusalemu kuti abweretse kwa Yehova msonkho wopatulika+ umene Mose mtumiki wa Mulungu woona analamula Aisiraeli mʼchipululu.