2 Mbiri 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Akalonga onse ndi anthu onse anasangalala,+ ndipo ankabweretsa ndalama za msonkhowo nʼkumaziponya mʼbokosi lija mpaka linadzaza.*
10 Akalonga onse ndi anthu onse anasangalala,+ ndipo ankabweretsa ndalama za msonkhowo nʼkumaziponya mʼbokosi lija mpaka linadzaza.*