2 Mbiri 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo anasiya nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo awo nʼkuyamba kutumikira mizati yopatulika* ndiponso mafano. Choncho Mulungu anakwiyira kwambiri Yuda ndi Yerusalemu chifukwa cha kulakwa kwawoko.
18 Iwo anasiya nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo awo nʼkuyamba kutumikira mizati yopatulika* ndiponso mafano. Choncho Mulungu anakwiyira kwambiri Yuda ndi Yerusalemu chifukwa cha kulakwa kwawoko.