2 Mbiri 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova anapitiriza kuwatumizira aneneri kuti awathandize kubwerera kwa iye. Aneneriwo anapitiriza kuwachenjeza, koma sanamvere.+
19 Yehova anapitiriza kuwatumizira aneneri kuti awathandize kubwerera kwa iye. Aneneriwo anapitiriza kuwachenjeza, koma sanamvere.+