2 Mbiri 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho Mfumu Yehoasi sanakumbukire chikondi chokhulupirika chimene Yehoyada bambo a Zekariya anamusonyeza ndipo anapha mwana wawo, yemwe pakufa ananena kuti: “Yehova aone zimene mwachitazi nʼkukubwezerani.”+
22 Choncho Mfumu Yehoasi sanakumbukire chikondi chokhulupirika chimene Yehoyada bambo a Zekariya anamusonyeza ndipo anapha mwana wawo, yemwe pakufa ananena kuti: “Yehova aone zimene mwachitazi nʼkukubwezerani.”+