-
2 Mbiri 25:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako Amaziya anasonkhanitsa Ayuda nʼkuwauza kuti aime motsatira nyumba za makolo awo. Anawaika mʼmagulu a anthu 1,000 ndiponso mʼmagulu a anthu 100 limodzi ndi atsogoleri awo, a mafuko a Yuda ndi Benjamini.+ Iye anawalemba mayina anthuwo, kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo+ ndipo anapeza kuti panali asilikali ophunzitsidwa bwino* komanso oyenera kupita kunkhondo okwana 300,000, oti angathe kunyamula mkondo waungʼono ndi chishango chachikulu.
-