2 Mbiri 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma munthu wa Mulungu woona anapita kwa Amaziya nʼkumuuza kuti: “Inu mfumu, musalole kuti asilikali a Isiraeli apite nanu limodzi, chifukwa Yehova sali ndi Aisiraeli+ kapenanso mbadwa za Efuraimu.
7 Koma munthu wa Mulungu woona anapita kwa Amaziya nʼkumuuza kuti: “Inu mfumu, musalole kuti asilikali a Isiraeli apite nanu limodzi, chifukwa Yehova sali ndi Aisiraeli+ kapenanso mbadwa za Efuraimu.