2 Mbiri 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Amaziya anafunsa munthu wa Mulungu woonayo kuti: “Nanga matalente 100 amene ndapereka kwa asilikali a ku Isiraeli aja?” Munthu wa Mulungu woonayo anayankha kuti: “Yehova akhoza kukupatsani zambiri kuposa zimenezo.”+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:9 Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu,5/2023, tsa. 7
9 Ndiyeno Amaziya anafunsa munthu wa Mulungu woonayo kuti: “Nanga matalente 100 amene ndapereka kwa asilikali a ku Isiraeli aja?” Munthu wa Mulungu woonayo anayankha kuti: “Yehova akhoza kukupatsani zambiri kuposa zimenezo.”+