-
2 Mbiri 25:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Choncho Amaziya anauza asilikali amene anabwera kwa iye kuchokera ku Efuraimu aja kuti abwerere kwawo. Koma asilikaliwo anawakwiyira kwambiri Ayuda moti anabwerera kwawo atapsa mtima kwambiri.
-