-
2 Mbiri 25:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Panalinso anthu 10,000 amene Ayuda anawagwira amoyo. Anthu amenewa anapita nawo pathanthwe lomwe linali pamwamba kwambiri nʼkuyamba kuwaponya kuchokera pathanthwepo ndipo onsewo ananyenyekanyenyeka.
-