2 Mbiri 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma pobwerera kuchokera kokapha Aedomu, Amaziya anatenga milungu ya anthu a ku Seiri nʼkukaiika pamalo ena kuti ikhale milungu yake.+ Kenako anayamba kuigwadira ndiponso kupereka nsembe zautsi kwa milunguyo.
14 Koma pobwerera kuchokera kokapha Aedomu, Amaziya anatenga milungu ya anthu a ku Seiri nʼkukaiika pamalo ena kuti ikhale milungu yake.+ Kenako anayamba kuigwadira ndiponso kupereka nsembe zautsi kwa milunguyo.