2 Mbiri 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Amaziya sanamvere,+ popeza Mulungu woona ndi amene anachititsa zimenezi kuti awapereke mʼmanja mwa adani,+ chifukwa iwo anatsatira milungu ya Edomu.+
20 Koma Amaziya sanamvere,+ popeza Mulungu woona ndi amene anachititsa zimenezi kuti awapereke mʼmanja mwa adani,+ chifukwa iwo anatsatira milungu ya Edomu.+