2 Mbiri 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Yehoasi, mfumu ya Isiraeli, anapita ndipo iye ndi Amaziya mfumu ya Yuda anakumana nʼkuyamba kumenyana ku Beti-semesi+ mʼdziko la Yuda.
21 Choncho Yehoasi, mfumu ya Isiraeli, anapita ndipo iye ndi Amaziya mfumu ya Yuda anakumana nʼkuyamba kumenyana ku Beti-semesi+ mʼdziko la Yuda.