-
2 Mbiri 25:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Yehoasi mfumu ya Isiraeli anagwira Amaziya mfumu ya Yuda mwana wa Yehoasi, mwana wa Yehoahazi* ku Beti-semesiko. Kenako Yehoasi anatenga Amaziya nʼkupita naye ku Yerusalemu ndipo anakagumula mpanda wa Yerusalemu kuyambira pa Geti la Efuraimu+ mpaka pa Geti la Pakona.+ Anagumula mpata waukulu pafupifupi mamita 178.*
-