2 Mbiri 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yehoasi anatenga golide ndi siliva yense komanso ziwiya zonse zimene anazipeza mʼnyumba ya Mulungu woona ndi* Obedi-edomu ndiponso chuma cha mʼnyumba ya mfumu.+ Anagwiranso anthu ena ndipo kenako anabwerera ku Samariya.
24 Yehoasi anatenga golide ndi siliva yense komanso ziwiya zonse zimene anazipeza mʼnyumba ya Mulungu woona ndi* Obedi-edomu ndiponso chuma cha mʼnyumba ya mfumu.+ Anagwiranso anthu ena ndipo kenako anabwerera ku Samariya.