2 Mbiri 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uziya+ anakhala mfumu ali ndi zaka 16, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 52. Amayi ake anali a ku Yerusalemu ndipo dzina lawo linali Yekoliya.+
3 Uziya+ anakhala mfumu ali ndi zaka 16, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 52. Amayi ake anali a ku Yerusalemu ndipo dzina lawo linali Yekoliya.+