2 Mbiri 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anapita kukamenyana ndi Afilisiti+ ndipo anagumula mpanda wa ku Gati,+ wa ku Yabine+ ndi wa ku Asidodi. Kenako anamanga mizinda mʼchigawo cha Asidodi+ ndiponso pakati pa Afilisiti.
6 Iye anapita kukamenyana ndi Afilisiti+ ndipo anagumula mpanda wa ku Gati,+ wa ku Yabine+ ndi wa ku Asidodi. Kenako anamanga mizinda mʼchigawo cha Asidodi+ ndiponso pakati pa Afilisiti.