15 Komanso ku Yerusalemu iye anapangako makina ankhondo opangidwa ndi anthu aluso. Makinawa anawaika pansanja+ ndi mʼmakona a mpanda ndipo ankatha kuponya mivi ndi miyala ikuluikulu. Choncho anatchuka kulikonse, chifukwa ankathandizidwa kwambiri ndipo anakhala wamphamvu.