2 Mbiri 26:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako Uziya, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake, koma anamuika kunja kwa manda a mafumu chifukwa anati: “Ndi wakhate.” Ndiyeno mwana wake Yotamu+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.
23 Kenako Uziya, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake, koma anamuika kunja kwa manda a mafumu chifukwa anati: “Ndi wakhate.” Ndiyeno mwana wake Yotamu+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.