2 Mbiri 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komanso anamanga mizinda+ mʼdera lamapiri la Yuda+ ndipo mʼdera lankhalango anamangamo nsanja+ ndiponso malo okhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+
4 Komanso anamanga mizinda+ mʼdera lamapiri la Yuda+ ndipo mʼdera lankhalango anamangamo nsanja+ ndiponso malo okhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+