2 Mbiri 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nkhani zina zokhudza Yotamu, zimene anachita komanso nkhondo zonse zomwe anamenya, zinalembedwa mʼBuku la Mafumu a Isiraeli ndi Yuda.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:7 Nsanja ya Olonda,3/15/2009, tsa. 32
7 Nkhani zina zokhudza Yotamu, zimene anachita komanso nkhondo zonse zomwe anamenya, zinalembedwa mʼBuku la Mafumu a Isiraeli ndi Yuda.+