2 Mbiri 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma anayenda mʼnjira za mafumu a Isiraeli+ ndipo anafika mpaka popanga zifaniziro zachitsulo+ za Abaala.
2 Koma anayenda mʼnjira za mafumu a Isiraeli+ ndipo anafika mpaka popanga zifaniziro zachitsulo+ za Abaala.