2 Mbiri 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kuwonjezera pamenepo, Ahazi anapereka nsembe yautsi mʼChigwa cha Mwana wa Hinomu.* Iye anawotcha ana ake pamoto+ potsatira zinthu zonyansa zimene ankachita anthu a mitundu ina+ amene Yehova anawathamangitsa pamaso pa Aisiraeli.
3 Kuwonjezera pamenepo, Ahazi anapereka nsembe yautsi mʼChigwa cha Mwana wa Hinomu.* Iye anawotcha ana ake pamoto+ potsatira zinthu zonyansa zimene ankachita anthu a mitundu ina+ amene Yehova anawathamangitsa pamaso pa Aisiraeli.