2 Mbiri 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Peka+ mwana wa Remaliya anapha anthu 120,000 ku Yuda tsiku limodzi ndipo onsewa anali amuna olimba mtima. Iwo anaphedwa chifukwa chakuti anasiya Yehova Mulungu wa makolo awo.+
6 Peka+ mwana wa Remaliya anapha anthu 120,000 ku Yuda tsiku limodzi ndipo onsewa anali amuna olimba mtima. Iwo anaphedwa chifukwa chakuti anasiya Yehova Mulungu wa makolo awo.+