-
2 Mbiri 28:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Yehova anatsitsa Ayuda chifukwa cha Ahazi mfumu ya Isiraeli, popeza analekerera Ayuda kuchita makhalidwe oipa zomwe zinachititsa kuti achite zinthu zambiri zosakhulupirika kwa Yehova.
-