2 Mbiri 28:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ahazi anali atatenga zinthu za mʼnyumba ya Yehova, za mʼnyumba ya mfumu+ ndi zamʼnyumba za akalonga nʼkuzipereka ngati mphatso kwa mfumu ya Asuri, koma zimenezi sizinamuthandize.
21 Ahazi anali atatenga zinthu za mʼnyumba ya Yehova, za mʼnyumba ya mfumu+ ndi zamʼnyumba za akalonga nʼkuzipereka ngati mphatso kwa mfumu ya Asuri, koma zimenezi sizinamuthandize.