2 Mbiri 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Anamanga malo okwezeka operekera nsembe zautsi kwa milungu ina+ mʼmizinda yonse ya Yuda ndipo anakwiyitsa Yehova Mulungu wa makolo ake.
25 Anamanga malo okwezeka operekera nsembe zautsi kwa milungu ina+ mʼmizinda yonse ya Yuda ndipo anakwiyitsa Yehova Mulungu wa makolo ake.